Mawu a M'munsi
a Anthu monga Baruki (mlembi wa Yeremiya), Ebedi-meleki Mwitiyopiya komanso Arekabu anapulumuka ngakhale kuti sanalembedwe chizindikiro chooneka. (Yer. 35:1-19; 39:15-18; 45:1-5) Iwo analembedwa chizindikiro chophiphiritsa pamphumi zawo.