Mawu a M'munsi
a Kachilembo kakang’ono ka afabeti yachigiriki ndi iota ndipo kayenera kuti kuchepa kwake n’kofanana ndi kachiheberi kaja י (yod). Popeza poyamba Chilamulo cha Mose chinalembedwa m’Chiheberi ndipo anthu ankachiwerenganso m’Chiheberi, apa Yesu ayenera kuti ankanena za kachilembo kachiheberi.