Mawu a M'munsi a Zimene Hana analonjezazi zinkatanthauza kuti mwana wakeyo adzakhala Mnaziri kwa moyo wake wonse. Zinkatanthauzanso kuti mwanayo adzakhala wosiyana ndi ana ena, adzaperekedwa kwa Yehova ndipo azidzachita utumiki wopatulika.—Num. 6:2, 5, 8.