Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Mkhristu angasankhe kukhala ndi mfuti kuti azigwiritsa ntchito posaka kapena podziteteza ku nyama zolusa. Koma zingakhale bwino kusunga mfutiyo pamalo obisika ilibe zipolopolo kapena ili yomasula. M’mayiko amene amaletsa kukhala ndi mfuti kapena salola kukhala nayo chisawawa, Akhristu ayenera kutsatira malamulowo.​—Aroma 13:1.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena