Mawu a M'munsi b Nowa anachitanso chimodzimodzi. Iye anali ndi mkazi mmodzi ngakhale kuti kukwatira mitala kunayamba pasanapite nthawi yaitali kuchokera pamene Adamu ndi Hava anachimwa.—Gen. 4:19.