Mawu a M'munsi
a Ngati mukufuna kudziwa mfundo zoyenera kutsatira pogwiritsa ntchito webusaiti yathu, pitani m’munsi mwenimweni pa jw.org pamene alemba kuti Zoyenera Kutsatira. Zinthu zimene talemba kuti simuyenera kuchita zikukhudza chilichonse chimene timaika pawebusaitiyi.