Mawu a M'munsi
a Kavinidwe kamene tikunena apa ndi koti wovinayo savala kwenikweni ndipo amakhalira kasitomala pantchafu n’kumamunyekulira. Koma malinga ndi zimene zachitika, zinthu ngati zimenezi zikhoza kukhala dama ndipo pangafunike komiti yoweruza. Mkhristu amene wachita zimenezi afunika kupempha thandizo kwa akulu.—Yak. 5:14, 15.