Mawu a M'munsi
a Kodi mawu oti mtima wosagawanika amatanthauza chiyani? N’chifukwa chiyani Yehova amafuna kuti tikhale nawo? Nanga n’chifukwa chiyani mtima wosagawanika ndi wofunika kwambiri? Nkhaniyi itithandiza kupeza mayankho a mafunsowa m’Baibulo. Itithandizanso kudziwa zimene tingachite kuti tizikhala ndi mtima wosagawanika nthawi zonse. Tikamachita zimenezi tidzapeza madalitso ambiri.