Mawu a M'munsi
a Tonsefe sitibadwa ndi mtima wofatsa moti timachita kuphunzira. Tikhoza kukhala ofatsa pochita zinthu ndi anthu amtendere koma zingativute tikamachita zinthu ndi anthu odzikuza. Munkhaniyi tikambirana zimene zingatithandize kuti tikhale anthu ofatsa.