Mawu a M'munsi
a N’chifukwa chiyani tinganene kuti tikamasonyeza chifundo, tikhoza kumasangalala mu utumiki ndipo zinthu zingamatiyendere bwino? Munkhaniyi tikambirana chitsanzo cha Yesu pa nkhani yosonyeza chifundo. Kenako tiona mmene ifeyo tingasonyezere chifundo kwa anthu amene timawalalikira.