Mawu a M'munsi
b TANTHAUZO LA MAWU ENA: Munkhaniyi, mawu oti chifundo akutanthauza kuganizira mmene munthu wina akumvera chifukwa cha mavuto kapena kuzunzidwa. Chifundo choterechi chimapangitsa munthu kuchita chilichonse chimene angathe kuti athandize anthu.