Mawu a M'munsi
a Tonsefe timakumana ndi mavuto amene angatilepheretse kukhala ndi mtendere mumtima. Munkhaniyi tikambirana zinthu zitatu zimene Yesu ankachita zomwe zingatithandize kukhala ndi mtendere ngakhale pamene tikukumana ndi mavuto aakulu.