Mawu a M'munsi
a Chifukwa chotikonda, Yehova watichenjeza za mizimu yoipa komanso mmene ingatisocheretsere. Kodi mizimu yoipa imasocheretsa bwanji anthu? Nanga tingalimbane nayo bwanji? Munkhaniyi tikambirana mmene Yehova amatithandizira kuti tisasocheretsedwe.