Mawu a M'munsi
a Nkhaniyi komanso nkhani ziwiri zotsatira zifotokoza mfundo zotitsimikizira kuti Yehova ndi Mulungu wachikondi komanso wachilungamo. Iye amafuna kuti anthu ake azichitiridwa zinthu zachilungamo ndipo amalimbikitsa anthu amene achitiridwa zinthu zopanda chilungamo mādziko loipali.