Mawu a M'munsi
e MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Yesu akudya kunyumba ya Mfarisi wina dzina lake Simoni. Mzimayi wina, yemwe mwina ndi hule, wasambitsa mapazi a Yesu ndi misozi yake ndipo wawapukuta ndi tsitsi lake n’kuwapaka mafuta. Simoni sakusangalala ndi zimene mzimayiyo wachita koma Yesu akumuikira kumbuyo.