Mawu a M'munsi
a Tikamada nkhawa kwambiri kapena kwa nthawi yaitali tikhoza kudwala komanso kusokonezeka maganizo. Ndiye kodi Yehova angatithandize bwanji? Tikambirana zimene Yehova anachita pothandiza Eliya pamene anali ndi nkhawa. Tikambirananso zitsanzo zina za m’Baibulo zimene zingatithandize kuti tizidalira Yehova tikakhala ndi nkhawa.