Mawu a M'munsi
f Tiyeneranso kupewa magulu monga a achinyamata kapena a masewera amene amakhudzana ndi zipembedzo zonyenga. Mwachitsanzo, tiyenera kupewa kukhala m’mabungwe a achinyamata monga a YMCA (Young Men’s Christian Association) kapena YWCA (Young Women’s Christian Association) omwe amanena kuti zochita zawo si zachipembedzo kwenikweni. Koma zoona zake n’zakuti mabungwe amenewa anayambitsidwa ndi zipembedzo komanso amalimbikitsa mfundo zachipembedzo.