Mawu a M'munsi
a Nkhaniyi ikusonyeza mmene mzimu woyera wa Mulungu ungatithandizire kuti tizipirira. Ifotokozanso zimene tingachite kuti mzimu woyera uzitithandiza kwambiri.