Mawu a M'munsi b Pa olemba mabuku a Uthenga Wabwino onse, Luka ndi amene anasonyeza kwambiri kuti Yesu ankakonda kupemphera.—Luka 3:21; 5:16; 6:12; 9:18, 28, 29; 18:1; 22:41, 44.