Mawu a M'munsi
a Mtumwi Paulo anakumana ndi mavuto ambiri pa moyo wake. Koma panali antchito anzake ena amene ankamuthandiza komanso kumulimbikitsa kwambiri. Munkhaniyi tikambirana makhalidwe atatu amene anathandiza anthuwo kuti akhale olimbikitsa. Tikambirananso zimene tingachite powatsanzira.