Mawu a M'munsi
a Chaka chino, mwambo wokumbukira imfa ya Khristu udzachitika Lachiwiri pa April 7. Kodi tiyenera kuwaona bwanji anthu amene adzadye zizindikiro? Kodi tiyenera kudandaula ngati odya zizindikiro akuwonjezereka? Munkhaniyi tipeza mayankho a mafunso amenewa ndipo mfundo zake zikugwirizana ndi za mu Nsanja ya Olonda ya January 2016.