Mawu a M'munsi
a M’gulu la Yehova muli mtendere. Koma ngati titayamba mtima wansanje, mtendere umenewu ukhoza kusokonekera. Munkhaniyi tikambirana zinthu zimene zingayambitse nsanje. Kenako tidzakambirana zimene tingachite kuti tipewe mtima umenewu n’kumalimbikitsa mtendere.