Mawu a M'munsi
a Yesu ananena kuti chikondi ndi chizindikiro cha Akhristu oona. Kukonda abale ndi alongo athu kumatithandiza kuti tizikhazikitsa mtendere, tikhale opanda tsankho komanso tizicherezana. Koma nthawi zina zimenezi zimakhala zovuta. Munkhaniyi tikambirana mfundo zimene zingatithandize kuti tipitirize kukondana kwambiri kuchokera mumtima.