Mawu a M'munsi
a Kwa zaka zambiri, takhala tikukhulupirira kuti ulosi wa m’chaputala 1 ndi 2 cha buku la Yoweli umalosera za ntchito yathu yolalikira yamasiku ano. Koma pali zifukwa 4 zomveka zochititsa kuti tisinthe kafotokozedwe ka ulosi umenewu. Kodi zifukwa zake ndi ziti?