Mawu a M'munsi
a Mu nkhani yapitayi, tinakambirana zinthu zingapo zomwe Mulungu anatipatsa zimene tingathe kuziona. Koma mu nkhaniyi, tikambirana zinthu zomwe sitingathe kuziona. Tikambirananso zimene tingachite poyamikira zinthu zimenezi komanso poyamikira Yehova Mulungu yemwe amatipatsa zinthuzi.