Mawu a M'munsi
a Pamene tikuyembekezera kuti malonjezo a Yehova akwaniritsidwe, tikhoza kutopa kapena chikhulupiriro chathu chingayambe kuchepa. Kodi tingaphunzire chiyani kwa Abulahamu pa nkhani ya kuyembekezera moleza mtima kukwaniritsidwa kwa malonjezo a Yehova? Nanga tingaphunzire chiyani kwa atumiki a Yehova ena a masiku ano?