Mawu a M'munsi
b MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Munthu amene anamwalira zaka zambiri zapitazo, waukitsidwa mu Ulamuliro wa Zaka 1,000 wa Khristu. M’bale amene wapulumuka pa Aramagedo, akumuphunzitsa zimene ayenera kuchita kuti apindule ndi nsembe ya Khristu.