Mawu a M'munsi
c MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: M’bale akufotokozera bwana wake kuti masiku ena mkati mwa mlungu sazigwira ovataimu. Iye akuuza abwana akewo kuti pa masiku amenewa amachita zinthu zina zokhudza kulambira Yehova. Koma ngati angafunike kwambiri masiku ena, akhoza kugwira ovataimu.