Mawu a M'munsi
a The Finished Mystery linali voliyumu ya nambala 7 ya buku lakuti Studies in the Scriptures. Buku lachikuto chofewa lomwe linkatchedwa kuti “ZG” linasindikizidwa ngati Nsanja ya Olonda ya March 1, 1918. Chilembo cha “Z” chinkaimira Zion’s Watch Tower ndipo chilembo cha “G” chomwe ndi cha nambala 7 mu afabeti, chinkaimira voliyumu nambala 7.