Mawu a M'munsi
b TANTHAUZO LA MAWU ENA: Ngati nthawi ndi nthawi mumakambirana ndi munthu mfundo za m’Baibulo pogwiritsa ntchito buku linalake, ndiye kuti mukuchititsa phunziro la Baibulo. Muyenera kuwerengera phunzirolo ngati mwaphunzira maulendo awiri kuchokera pamene munamusonyeza mmene timaphunzirira ndiponso ngati mukuona kuti phunzirolo likhoza kupitirira.