Mawu a M'munsi
a Tikamaphunzira Baibulo ndi anthu, timakhala ndi mwayi woti tiwathandize kuti ayambe kuganiza komanso kuchita zinthu m’njira imene Yehova amafuna. Nkhaniyi ikufotokoza zinthu zinanso zimene zingatithandize kuti tikhale aphunzitsi aluso.