Mawu a M'munsi
a Munkhaniyi tikambirana njira zitatu zimene Yehova anathandizira mtumwi Paulo kuti apirire mavuto amene anakumana nawo. Kukambirana mmene Yehova anathandizira atumiki ake ena m’mbuyomu, kutithandiza kuti tizikhulupirira kwambiri kuti Yehova azitithandizanso masiku ano tikamakumana ndi mavuto.