Mawu a M'munsi
b Mawu amenewa amapezeka m’Baibulo Lopatulika pa Agalatiya 6:7. Anthu akum’mawa kwa dziko lapansi amakonda kufotokoza mfundo yamulembali kuti ukadzala mavwende, udzakololanso mavwende; ukadzala nyemba, udzakololanso nyemba.