Mawu a M'munsi
b Nthawi zina mabuku, mafilimu kapena masewero, amasonyeza kuti palibe vuto ngati mwamuna atamachitira nkhanza kapena kuzunza mkazi wake. Maganizo amenewa amachititsa kuti anthu ambiri aziona kuti sikulakwa kuti mwamuna azipondereza mkazi wake.