Mawu a M'munsi
a Yehova anakonza zoti mkazi wokwatiwa azigonjera mwamuna wake. Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani? Amuna a Chikhristu ndi akazi awo, angaphunzire zambiri pa nkhani yokhala ogonjera pa chitsanzo cha Yesu komanso akazi ena omwe nkhani zawo zinalembedwa m’Baibulo.