Mawu a M'munsi
a Kodi Yehova anapatsa alongo ntchito yotani mumpingo? Kodi m’bale aliyense amakhala mutu wa mlongo aliyense mumpingo? Kodi udindo wa akulu mumpingo ndi wofanana ndi wa mitu ya mabanja? Munkhaniyi, tiona mmene Baibulo litithandizire kupeza mayankho a mafunsowa.