Mawu a M'munsi
a Si tonse amene panopa tili ndi mwayi wochititsa phunziro la Baibulo. Komabe, aliyense mumpingo angathandize kuti winawake abatizidwe. Munkhaniyi tiona zimene tingachite kuti tizithandiza ophunzira Baibulo kuti afike pobatizidwa.