Mawu a M'munsi
a Tikukhala mu nthawi yovuta kwambiri, koma Yehova amatithandiza kupirira. Munkhaniyi tikambirana mmene anathandizira mtumwi Paulo ndi Timoteyo kuti apitirizebe kumutumikira ngakhale kuti ankakumana ndi mavuto. Tikambirananso zinthu 4 zimene Yehova watipatsa kuti tithe kupirira masiku ano.