Mawu a M'munsi
a Kodi nthawi zina mumalimbana ndi maganizo odziona ngati muli nokhanokha? Ngati ndi choncho, dziwani kuti Yehova amadziwa bwino mmene mumamvera ndipo amafunitsitsa kuti akuthandizeni. Munkhaniyi tikambirana zimene mungachite ngati mwayamba kukhala ndi maganizo odziona ngati muli nokhanokha. Tikambirananso mmene tingalimbikitsire Akhristu anzathu amene amadziona kuti ali okhaokha.