Mawu a M'munsi
a Satana ali ngati mlenje waluso. Iye amafuna kutikola m’misampha yake ngakhale titakhala kuti tatumikira Yehova kwa nthawi yaitali. Munkhaniyi tiona mmene iye amagwiritsira ntchito kunyada komanso dyera pofuna kusokoneza ubwenzi wathu ndi Yehova. Tionanso zimene tingaphunzirepo pa zitsanzo za anthu amene anakodwa mumsampha wakunyada komanso wadyera ndiponso zimene tingachite kuti tipewe misampha imeneyi.