Mawu a M'munsi
d MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Kunyada kunasokoneza mngelo wina wa Mulungu komanso Mfumu Uziya. Dyera linachititsa kuti Hava adye chipatso cha mumtengo woletsedwa, Davide achite chigololo ndi Batiseba komanso kuti Yudasi aziba ndalama.