Mawu a M'munsi
b MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Woyang’anira dera atakwanitsa zaka 70, iye ndi mkazi wake anapatsidwa utumiki watsopano. Zomwe anaphunzira pazaka zambiri zimene akhala akutumikira zimawathandiza kuphunzitsa ena mumpingo umene akutumikira panopa.