Mawu a M'munsi
a Kulapa kwenikweni kumaphatikizapo zambiri, osati kungonena kuti tikudzimvera chisoni chifukwa cha tchimo limene tachita. Pogwiritsa ntchito zitsanzo za Mfumu Ahabu, Mfumu Manase ndi mwana wolowerera wa m’fanizo la Yesu, nkhaniyi itithandiza kumvetsa zimene kulapa kwenikweni kumatanthauza. Tionanso mfundo zimene akulu ayenera kuganizira kuti adziwe ngati Mkhristu amene anachita tchimo lalikulu akusonyeza kulapa kwenikweni.