Mawu a M'munsi
a Munkhaniyi, tiziyerekekezera kuti amene wachita chigololoyo ndi mwamuna ndipo wosalakwayo ndi mkazi. Komabe pa Maliko 10:11, 12, Yesu anafotokoza momveka bwino kuti malangizo ake pa nkhaniyi, amakhudza onse, amuna ndi akazi omwe.