Mawu a M'munsi
a M’Mawu ake, Yehova amatitsimikizira kuti ndi wofunitsitsa kukhululukira anthu ochimwa omwe alapa. Koma nthawi zina tingamaone kuti si ife oyenera kuti atikhululukire. Munkhaniyi tiona chifukwa chake tingakhale otsimikiza kuti Mulungu wathu ndi wokonzeka kutikhululukira tikamadzimvera chisoni chifukwa cha machimo omwe tinachita.