Mawu a M'munsi
c TANTHAUZO LA MAWU ENA: “Kulapa” kumatanthauza kusintha maganizo komanso kudzimvera chisoni chifukwa cha zoipa zimene takhala tikuchita kapena chifukwa cholephera kuchita zoyenera. Kulapa kwenikweni kumakhala ndi zipatso zake, zomwe ndi kusintha mmene timachitira zinthu pa moyo wathu.