Mawu a M'munsi
a Tikukhala munthawi yosangalatsa kwambiri chifukwa Ufumu wa Mulungu unayamba kulamulira, monga mmene maulosi a m’Baibulo ananenera. Nkhaniyi ifotokoza ena mwa maulosiwa n’cholinga chofuna kutithandiza kuti tizikhulupirira kwambiri Yehova komanso kuti tizimudalira panopa ndiponso m’tsogolo.