Mawu a M'munsi
a Amuna, akazi komanso ana ambirimbiri akulalikira mwakhama uthenga wabwino. Kodi inunso ndi māmodzi wa anthu amenewa? Ngati ndi choncho, dziwani kuti mukugwira nawo ntchito yomwe Ambuye wathu Yesu Khristu akutsogolera. Munkhaniyi, tiona umboni wosonyeza kuti Yesu akutsogolera ntchito yolalikirayi. Kuganizira zimenezi kutithandiza kuti tikhale otsimikiza kupitiriza kutumikira Yehova motsogoleredwa ndi Khristu.