Mawu a M'munsi
a Timayamikira kwambiri mwayi wopemphera kwa Yehova. Timafuna kuti mapemphero athu azikhala ngati zofukiza zonunkhira bwino, zomwe zingamusangalatse. Munkhaniyi, tikambirana zimene tingatchule m’mapemphero athu. Tikambirananso mfundo zina zimene tiyenera kukumbukira tikapemphedwa kuti tiimire anthu ena m’pemphero.