Mawu a M'munsi
a Timafunika kuthandizidwa ndi Yehova kuti tikwanitse kulimbana ndi mavuto amene timakumana nawo masiku ano. Nkhaniyi ititsimikizira kuti Yehova amayang’anira anthu ake. Iye amaona mavuto amene aliyense akukumana nawo ndipo amatipatsa zomwe timafunikira kuti tithe kupirira.